5 Muzisunga mfundo zanga ndi zigamulo zanga, zimene ngati munthu azitsatira adzakhaladi ndi moyo chifukwa cha mfundo ndi zigamulo zimenezo.+ Ine ndine Yehova.+
13 Ndiyeno munatsikira paphiri la Sinai+ ndi kulankhula nawo muli kumwamba.+ Munawapatsa zigamulo zowongoka+ ndi malamulo a choonadi,+ mfundo zabwino ndi malangizo abwino.+