Salimo 97:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ziyoni anamva ndipo anayamba kusangalala,+Midzi yozungulira Yuda inayamba kukondwera+Chifukwa cha zigamulo zanu, inu Yehova.+ Chivumbulutso 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+
8 Ziyoni anamva ndipo anayamba kusangalala,+Midzi yozungulira Yuda inayamba kukondwera+Chifukwa cha zigamulo zanu, inu Yehova.+
2 chifukwa ziweruzo zake ndi zoona ndi zolungama.+ Pakuti iye waweruza hule lalikulu limene linaipitsa dziko lapansi ndi dama* lake, ndipo walibwezera chifukwa cha magazi a akapolo ake, amene hulelo linapha.”+