Salimo 55:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usiku, m’mawa ndi masana ndimakhala ndi nkhawa ndipo ndimakhala ndikulira,+Choncho Mulungu amamva mawu anga.+ Salimo 119:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Pakati pa usiku ndimadzuka kuti ndikuyamikeni+Chifukwa cha zigamulo zanu zolungama.+
17 Usiku, m’mawa ndi masana ndimakhala ndi nkhawa ndipo ndimakhala ndikulira,+Choncho Mulungu amamva mawu anga.+