Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 7:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Nthawi yomweyo Mose ndi Aroni anachita zomwezo,+ monga momwe Yehova anawalamulira.+ Ndipo Aroni anatenga ndodo yake ndi kumenya madzi a mumtsinje wa Nailo, Farao ndi atumiki ake akuona.+ Pamenepo madzi onse a mumtsinje wa Nailo anasanduka magazi.+

  • 2 Mbiri 29:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 M’chaka choyamba cha ulamuliro wake, m’mwezi woyamba,* iye anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova n’kuyamba kuzikonza.+

  • Machitidwe 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Mu ola lomwelo la usiku, anawatenga ndi kuwatsuka zilonda zawo. Ndipo onse, iye ndi a m’banja lake, anabatizidwa+ mosataya nthawi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena