Machitidwe 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iwo atakhulupirira Filipo, amene anali kulengeza uthenga wabwino wonena za ufumu wa Mulungu+ ndi za dzina la Yesu Khristu, anabatizidwa, amuna ndi akazi omwe.+ Machitidwe 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+
12 Koma iwo atakhulupirira Filipo, amene anali kulengeza uthenga wabwino wonena za ufumu wa Mulungu+ ndi za dzina la Yesu Khristu, anabatizidwa, amuna ndi akazi omwe.+
15 Tsopano iye ndi a m’banja lake atabatizidwa,+ anachonderera kuti: “Abale ngati inu mwaona kuti ndine wokhulupirika kwa Yehova, tiyeni mukalowe m’nyumba yanga ndi kukhala mmenemo.”+ Moti anatiumiriza ndithu kupita kwawo.+