Ezekieli 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu onse omuzungulira amene amamuthandiza, ndiponso magulu ake onse ankhondo, ndidzawabalalitsira ku mphepo zonse zinayi,+ ndipo ndidzawatsatira nditasolola lupanga.+
14 Anthu onse omuzungulira amene amamuthandiza, ndiponso magulu ake onse ankhondo, ndidzawabalalitsira ku mphepo zonse zinayi,+ ndipo ndidzawatsatira nditasolola lupanga.+