Ezekieli 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu onse amene amuzungulira, amene amamuthandiza ndiponso asilikali ake, ndidzawabalalitsira kumbali zonse+ ndipo ndidzasolola lupanga kuti ndiwathamangitse.+
14 Anthu onse amene amuzungulira, amene amamuthandiza ndiponso asilikali ake, ndidzawabalalitsira kumbali zonse+ ndipo ndidzasolola lupanga kuti ndiwathamangitse.+