-
Yeremiya 42:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 imvani mawu a Yehova, inu otsala a Yuda. Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ngati mwatsimikiza mtima kuti mupite ku Iguputo ndipo mukapitadi nʼkukakhala* kumeneko, 16 ndiye kuti lupanga limene mukuliopa lidzakupezani ku Iguputo komweko ndipo njala imene mukuiopa idzakutsatirani ku Iguputoko moti mudzafera komweko.+
-