Yeremiya 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndiye kuti lupanga limene mukuliopa lidzakupezani ku Iguputo+ komweko ndipo njala yaikulu imene mukuithawa idzakutsatirani ku Iguputoko+ moti mudzafera komweko.+
16 ndiye kuti lupanga limene mukuliopa lidzakupezani ku Iguputo+ komweko ndipo njala yaikulu imene mukuithawa idzakutsatirani ku Iguputoko+ moti mudzafera komweko.+