Deuteronomo 28:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 “Matemberero onsewa+ adzakugwera, kukutsatira ndi kukupeza kufikira utafafanizika,+ chifukwa sunamvere mawu a Yehova Mulungu wako mwa kusunga malamulo ndi mfundo zake zimene anakupatsa.+ Miyambo 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsoka limatsatira ochimwa,+ koma olungama ndi amene amalandira mphoto zabwino.+ Ezekieli 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Inu mukuopa lupanga,+ koma ine ndidzakubweretserani lupanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+
45 “Matemberero onsewa+ adzakugwera, kukutsatira ndi kukupeza kufikira utafafanizika,+ chifukwa sunamvere mawu a Yehova Mulungu wako mwa kusunga malamulo ndi mfundo zake zimene anakupatsa.+
8 “‘Inu mukuopa lupanga,+ koma ine ndidzakubweretserani lupanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+