Levitiko 26:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 pamenepo ndidzatsutsana nanu koopsa,+ ndipo ineyo ndidzakukwapulani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+ 2 Mafumu 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+ Yesaya 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma mukakana+ n’kupanduka, mudzawonongedwa ndi lupanga, chifukwa pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+ Yeremiya 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzawatumizira lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri,+ kufikira adzatheratu m’dziko limene ndinawapatsa, iwowo ndi makolo awo.”’”+
28 pamenepo ndidzatsutsana nanu koopsa,+ ndipo ineyo ndidzakukwapulani maulendo 7 chifukwa cha machimo anu.+
20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+
20 Koma mukakana+ n’kupanduka, mudzawonongedwa ndi lupanga, chifukwa pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+
10 Ndidzawatumizira lupanga,+ njala yaikulu+ ndi mliri,+ kufikira adzatheratu m’dziko limene ndinawapatsa, iwowo ndi makolo awo.”’”+