Levitiko 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Koma ngati simudzandimverabe pambuyo poona zinthu zimenezi, pamenepo ndidzakulangani mowirikiza ka 7 kuposa poyamba chifukwa cha machimo anu.+ Levitiko 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+
18 “‘Koma ngati simudzandimverabe pambuyo poona zinthu zimenezi, pamenepo ndidzakulangani mowirikiza ka 7 kuposa poyamba chifukwa cha machimo anu.+
21 “‘Koma mukapitirizabe kuchita zosemphana ndi zofuna zanga, osafuna kundimvera, pamenepo ndidzakukanthani mowirikiza ka 7 malinga ndi machimo anu.+