Yeremiya 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inauza Yeremiya kuti: “Ndikuopa Ayuda amene athawira kwa Akasidi.+ Ndikuopa kuti Akasidi andipereka m’manja mwawo ndipo Ayudawo andizunza.”+ Yeremiya 42:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+
19 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inauza Yeremiya kuti: “Ndikuopa Ayuda amene athawira kwa Akasidi.+ Ndikuopa kuti Akasidi andipereka m’manja mwawo ndipo Ayudawo andizunza.”+
14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+