-
Yeremiya 38:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inauza Yeremiya kuti: “Ndikuopa Ayuda amene athawira kwa Akasidi chifukwa ngati ndingaperekedwe mʼmanja mwawo akhoza kundizunza.”
-