Yeremiya 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inauza Yeremiya kuti: “Ndikuopa Ayuda amene athawira kwa Akasidi.+ Ndikuopa kuti Akasidi andipereka m’manja mwawo ndipo Ayudawo andizunza.”+
19 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inauza Yeremiya kuti: “Ndikuopa Ayuda amene athawira kwa Akasidi.+ Ndikuopa kuti Akasidi andipereka m’manja mwawo ndipo Ayudawo andizunza.”+