Yeremiya 44:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzalanga onse okhala m’dziko la Iguputo monga mmene ndinalangira Yerusalemu. Ndidzawalanga ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri.+ Yeremiya 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ine ndikhala tcheru kuti ndiwabweretsere tsoka osati zabwino.+ Ndipo anthu onse a ku Yuda amene ali m’dziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndi njala yaikulu kufikira atatheratu.+
13 Ndidzalanga onse okhala m’dziko la Iguputo monga mmene ndinalangira Yerusalemu. Ndidzawalanga ndi lupanga, njala yaikulu ndi mliri.+
27 Ine ndikhala tcheru kuti ndiwabweretsere tsoka osati zabwino.+ Ndipo anthu onse a ku Yuda amene ali m’dziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndi njala yaikulu kufikira atatheratu.+