Yeremiya 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndiye kuti lupanga limene mukuliopa lidzakupezani ku Iguputo komweko ndipo njala imene mukuiopa idzakutsatirani ku Iguputoko moti mudzafera komweko.+
16 ndiye kuti lupanga limene mukuliopa lidzakupezani ku Iguputo komweko ndipo njala imene mukuiopa idzakutsatirani ku Iguputoko moti mudzafera komweko.+