2 Mafumu 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Gulu lankhondo la Akasidi+ linayamba kuthamangitsa mfumuyo ndipo linaipeza+ m’chipululu cha Yeriko.+ Pamenepo gulu lonse lankhondo la mfumuyo linabalalika n’kuisiya yokha. Ezekieli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘“Choncho pakati pako, abambo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumphepo zonse zinayi.”’+ Ezekieli 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Gulu lonse la asilikali ake amene anathawa, lidzaphedwa ndi lupanga. Amene adzapulumuke adzabalalikira ku mphepo zonse.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine Yehova ndi amene ndanena zimenezi.”’+
5 Gulu lankhondo la Akasidi+ linayamba kuthamangitsa mfumuyo ndipo linaipeza+ m’chipululu cha Yeriko.+ Pamenepo gulu lonse lankhondo la mfumuyo linabalalika n’kuisiya yokha.
10 “‘“Choncho pakati pako, abambo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumphepo zonse zinayi.”’+
21 Gulu lonse la asilikali ake amene anathawa, lidzaphedwa ndi lupanga. Amene adzapulumuke adzabalalikira ku mphepo zonse.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine Yehova ndi amene ndanena zimenezi.”’+