Yeremiya 52:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linayamba kuthamangitsa mfumuyo+ ndipo Zedekiya anamupeza+ m’chipululu cha Yeriko. Zitatero gulu lonse lankhondo la Zedekiya linabalalika n’kumusiya yekha.+
8 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linayamba kuthamangitsa mfumuyo+ ndipo Zedekiya anamupeza+ m’chipululu cha Yeriko. Zitatero gulu lonse lankhondo la Zedekiya linabalalika n’kumusiya yekha.+