Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 30:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndipo munanena kuti: “Ayi, ife tidzakwera pamahatchi n’kuthawa!”+ N’chifukwa chake mudzathawe. Munanenanso kuti: “Tidzakwera pamahatchi othamanga kwambiri!”+ N’chifukwa chake anthu okuthamangitsani adzakhale othamanga kwambiri.+

  • Yeremiya 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Chotero mofanana ndi nkhuyu zoipa zija zimene munthu sangadye chifukwa cha kuipa kwake,+ Yehova wanena kuti: “Momwemonso ndidzapereka Zedekiya+ mfumu ya Yuda, akalonga ake ndi anthu onse opulumuka mu Yerusalemu amene atsalira m’dzikoli,+ komanso anthu okhala m’dziko la Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena