8 Koma mofanana ndi nkhuyu zoipa zija, zimene ndi zoipa kwambiri moti munthu sangathe kudya,+ Yehova wanena kuti: “Ndi mmenenso ndidzaonere Zedekiya+ mfumu ya Yuda, akalonga ake, anthu onse opulumuka mu Yerusalemu amene atsalira mʼdzikoli komanso anthu okhala mʼdziko la Iguputo.+