Yeremiya 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene ankakhala mʼdziko la Iguputo,+ mʼmadera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi*+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti: Yeremiya 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anauza mneneri Yeremiya zokhudza kubwera kwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo kudzaukira dziko la Iguputo. Iye anati:+
44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene ankakhala mʼdziko la Iguputo,+ mʼmadera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi*+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti:
13 Yehova anauza mneneri Yeremiya zokhudza kubwera kwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo kudzaukira dziko la Iguputo. Iye anati:+