Ezekieli 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aiguputo amene anagwidwa nʼkupita nawo kudziko lina ndidzawabwezeretsa ku Patirosi,+ mʼdziko limene anachokera ndipo kumeneko Iguputo adzakhala ufumu wonyozeka. Ezekieli 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani ndidzauwotcha ndi moto ndipo ndidzaweruza mzinda wa No.*+
14 Aiguputo amene anagwidwa nʼkupita nawo kudziko lina ndidzawabwezeretsa ku Patirosi,+ mʼdziko limene anachokera ndipo kumeneko Iguputo adzakhala ufumu wonyozeka.
14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani ndidzauwotcha ndi moto ndipo ndidzaweruza mzinda wa No.*+