Genesis 10:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Miziraimu anabereka Ludimu,+ Anamimu, Lehabimu, Nafituhimu,+ 14 Patirusimu,+ Kasiluhimu (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu) ndiponso Kafitorimu.+ Yeremiya 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene ankakhala mʼdziko la Iguputo,+ mʼmadera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi*+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti:
13 Miziraimu anabereka Ludimu,+ Anamimu, Lehabimu, Nafituhimu,+ 14 Patirusimu,+ Kasiluhimu (Afilisiti+ anachokera mwa iyeyu) ndiponso Kafitorimu.+
44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene ankakhala mʼdziko la Iguputo,+ mʼmadera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi*+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti: