Ezekieli 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, iwe ndikulanga ndipo ndiwononga mtsinje wako wa Nailo ndipo dziko la Iguputo ndiliwononga nʼkulisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ nʼkukafika kumalire a dziko la Itiyopiya. Ezekieli 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti: ‘Anthu amene akuthandiza Iguputo nawonso adzaphedwa,Ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga mʼdzikolo kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
10 Choncho, iwe ndikulanga ndipo ndiwononga mtsinje wako wa Nailo ndipo dziko la Iguputo ndiliwononga nʼkulisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ nʼkukafika kumalire a dziko la Itiyopiya.
6 Yehova wanena kuti: ‘Anthu amene akuthandiza Iguputo nawonso adzaphedwa,Ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga mʼdzikolo kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.