-
Ezekieli 30:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Yehova wanena kuti:
‘Anthu amene akuthandiza Iguputo nawonso adzaphedwa,
Ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.+
Anthu adzaphedwa ndi lupanga mʼdzikolo kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. 7 ‘Onsewo adzawonongeka kwambiri pa mayiko onse ndipo mizinda yawo idzakhala yowonongeka kwambiri pa mizinda yonse.+
-