Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 46:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Longedza katundu wako pokonzekera kupita ku ukapolo,

      Iwe mwana wamkazi amene ukukhala mu Iguputo.

      Chifukwa mzinda wa Nofi* udzakhala chinthu chochititsa mantha.

      Udzawotchedwa ndi moto* ndipo simudzapezeka aliyense wokhalamo.+

  • Ezekieli 29:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndidzachititsa kuti dziko la Iguputo likhale lowonongeka kwambiri kuposa mayiko ena onse, ndipo mizinda yake idzakhala yowonongeka kwambiri pa mizinda yonse kwa zaka 40.+ Ndidzamwaza Aiguputo pakati pa anthu a mitundu ina ndipo ndidzawabalalitsira mʼmayiko ena.”+

  • Ezekieli 32:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Iwe mwana wa munthu, lirira gulu la anthu onse a ku Iguputo ndipo utsitsire dzikolo kumanda. Utsitsire kumanda dzikolo ndi ana aakazi a mitundu yamphamvu limodzi ndi amene akutsikira kudzenje.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena