Yeremiya 46:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ‘Longedza katundu wopita naye ku ukapolo,+ iwe mwana wamkazi wokhala+ mu Iguputo. Pakuti mzinda wa Nofi+ udzakhala chinthu chodabwitsa ndipo adzautentha, moti simudzapezeka aliyense wokhalamo.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:19 Nsanja ya Olonda,7/1/2003, tsa. 32
19 ‘Longedza katundu wopita naye ku ukapolo,+ iwe mwana wamkazi wokhala+ mu Iguputo. Pakuti mzinda wa Nofi+ udzakhala chinthu chodabwitsa ndipo adzautentha, moti simudzapezeka aliyense wokhalamo.+