Yeremiya 48:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Tsika pamalo ako aulemerero ndipo ukhale ndi ludzu, iwe mwana wamkazi wokhala+ ku Diboni+ chifukwa wowononga Mowabu wabwera kudzakuukira. Iye adzasandutsa bwinja malo ako a mipanda yolimba kwambiri.+
18 “Tsika pamalo ako aulemerero ndipo ukhale ndi ludzu, iwe mwana wamkazi wokhala+ ku Diboni+ chifukwa wowononga Mowabu wabwera kudzakuukira. Iye adzasandutsa bwinja malo ako a mipanda yolimba kwambiri.+