Yeremiya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+ Yeremiya 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene anali kukhala m’dziko la Iguputo,+ m’madera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti: Yeremiya 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anauza mneneri Yeremiya mawu okhudza kubwera kwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo kudzaukira dziko la Iguputo.+ Iye anati:
7 Pamapeto pake anafika ku Iguputo+ chifukwa sanamvere mawu a Yehova ndipo patapita nthawi anakafika ku Tahapanesi.+
44 Mulungu anauza Yeremiya uthenga woti akauze Ayuda onse amene anali kukhala m’dziko la Iguputo,+ m’madera a Migidoli,+ Tahapanesi,+ Nofi+ ndi Patirosi.+ Uthengawo unali wakuti:
13 Yehova anauza mneneri Yeremiya mawu okhudza kubwera kwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo kudzaukira dziko la Iguputo.+ Iye anati: