-
Ezekieli 30:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndidzayatsa moto mu Iguputo. Sini adzamva ululu waukulu, No adzalandidwa ndi adani amene adzagumule mpanda wake. Adani adzalowa mumzinda wa Nofi masanasana.
-