Oweruza 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zitatero, atsogoleri a anthu ndi mafuko onse a Isiraeli anaimirira pakati pa mpingo wonse wa anthu a Mulungu woona.+ Amuna ogwira lupanga oyenda pansi analipo 400,000.+ 1 Samueli 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho Sauli ananena kuti: “Bwerani kuno,+ inu nonse atsogoleri a anthu,+ ndipo tifufuze ndi kudziwa mmene tchimoli lachitikira lero.
2 Zitatero, atsogoleri a anthu ndi mafuko onse a Isiraeli anaimirira pakati pa mpingo wonse wa anthu a Mulungu woona.+ Amuna ogwira lupanga oyenda pansi analipo 400,000.+
38 Choncho Sauli ananena kuti: “Bwerani kuno,+ inu nonse atsogoleri a anthu,+ ndipo tifufuze ndi kudziwa mmene tchimoli lachitikira lero.