Oweruza 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Amuna ogwira lupanga a mu Isiraeli amene anasonkhanitsidwa pamodzi anali 400,000,+ kupatulapo amuna a m’dera la Benjamini. Aliyense wa amenewa anali mwamuna wankhondo. 2 Samueli 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano Yowabu anapereka chiwerengero chonse+ cha anthu kwa mfumu. Aisiraeli analipo 800,000, amuna amphamvu ogwira lupanga, ndipo amuna a Yuda analipo 500,000.+ 2 Mafumu 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mfumu ya Mowabu itaona kuti nkhondo yaikulira, nthawi yomweyo inatenga amuna 700 amalupanga pofuna kudutsa kuti ikapeze mfumu ya Edomu,+ koma iwo analephera.
17 Amuna ogwira lupanga a mu Isiraeli amene anasonkhanitsidwa pamodzi anali 400,000,+ kupatulapo amuna a m’dera la Benjamini. Aliyense wa amenewa anali mwamuna wankhondo.
9 Tsopano Yowabu anapereka chiwerengero chonse+ cha anthu kwa mfumu. Aisiraeli analipo 800,000, amuna amphamvu ogwira lupanga, ndipo amuna a Yuda analipo 500,000.+
26 Mfumu ya Mowabu itaona kuti nkhondo yaikulira, nthawi yomweyo inatenga amuna 700 amalupanga pofuna kudutsa kuti ikapeze mfumu ya Edomu,+ koma iwo analephera.