Numeri 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Amenewa ndiwo anali olembedwa mayina a ana a Isiraeli, malinga ndi nyumba ya makolo awo. Asilikali onse olembedwa mayina m’misasa yonse, analipo 603,550.+ Numeri 26:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Amenewa ndiwo amuna onse amene anawerengedwa pakati pa ana a Isiraeli. Onse pamodzi analipo 601,730.+ 1 Mbiri 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Davide sanawerenge amuna amene anali ndi zaka 20 kutsika m’munsi, chifukwa Yehova analonjeza kuti adzachulukitsa Aisiraeli ngati nyenyezi zakumwamba.+
32 Amenewa ndiwo anali olembedwa mayina a ana a Isiraeli, malinga ndi nyumba ya makolo awo. Asilikali onse olembedwa mayina m’misasa yonse, analipo 603,550.+
51 Amenewa ndiwo amuna onse amene anawerengedwa pakati pa ana a Isiraeli. Onse pamodzi analipo 601,730.+
23 Davide sanawerenge amuna amene anali ndi zaka 20 kutsika m’munsi, chifukwa Yehova analonjeza kuti adzachulukitsa Aisiraeli ngati nyenyezi zakumwamba.+