Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 38:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mwamuna aliyense amene anawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita m’tsogolo,+ anapereka hafu ya sekeli lolingana ndi hafu ya sekeli la kumalo oyera. Owerengedwa onse anakwana 603,550.+

  • Numeri 1:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 onse amene analembedwa mayina anakwana 603,550.+

  • Numeri 1:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 “A fuko la Levi okha usawalembe mayina, ndipo usawawerengere pamodzi ndi ana a Isiraeli enawo.+

  • Numeri 2:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Amenewa ndiwo anali olembedwa mayina a ana a Isiraeli, malinga ndi nyumba ya makolo awo. Asilikali onse olembedwa mayina m’misasa yonse, analipo 603,550.+

  • Numeri 14:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+

  • Nehemiya 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndipo munawachulukitsira ana awo ngati nyenyezi zakumwamba.+ Mutatero munawalowetsa m’dziko+ limene munalonjeza makolo awo+ kuti akalowe ndi kulitenga.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena