Yoswa 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ansembe onyamula likasa la pangano la Yehova anangoima chilili panthaka youma+ pakati pa mtsinje wa Yorodano. Anaimabe choncho pamene Aisiraeli onse anali kuwoloka panthaka youmayo,+ kufikira mtundu wonse unatha kuwoloka mtsinje wa Yorodano.
17 Ansembe onyamula likasa la pangano la Yehova anangoima chilili panthaka youma+ pakati pa mtsinje wa Yorodano. Anaimabe choncho pamene Aisiraeli onse anali kuwoloka panthaka youmayo,+ kufikira mtundu wonse unatha kuwoloka mtsinje wa Yorodano.