Yoswa 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwalamule kuti, ‘Pitani pakati penipeni pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe anaimapo chilili,+ mukanyamulepo miyala 12.+ Muisenze ndi kukaiika kumene mugone+ usiku wa lero.’” 2 Mafumu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Eliya anatenga chovala chake chauneneri+ n’kuchipinda. Atatero anamenya nacho madzi a mtsinjewo, ndipo pang’onopang’ono madzi onsewo anagawanika uku ndi uku, chotero iwo anawoloka pouma.+
3 Uwalamule kuti, ‘Pitani pakati penipeni pa mtsinje wa Yorodano, pamalo amene ansembe anaimapo chilili,+ mukanyamulepo miyala 12.+ Muisenze ndi kukaiika kumene mugone+ usiku wa lero.’”
8 Kenako Eliya anatenga chovala chake chauneneri+ n’kuchipinda. Atatero anamenya nacho madzi a mtsinjewo, ndipo pang’onopang’ono madzi onsewo anagawanika uku ndi uku, chotero iwo anawoloka pouma.+