Yoswa 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthuwo anawoloka mtsinje wa Yorodano pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, ndipo anakamanga msasa ku Giligala,+ kumalire a kum’mawa kwa Yeriko. Yoswa 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Miyala 12 imene iwo anaitenga mumtsinje wa Yorodano ija, Yoswa anaisanjikiza ku Giligala.+
19 Anthuwo anawoloka mtsinje wa Yorodano pa tsiku la 10 la mwezi woyamba, ndipo anakamanga msasa ku Giligala,+ kumalire a kum’mawa kwa Yeriko.