-
1 Mafumu 19:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Chotero Eliya anachoka kumeneko n’kupita kwa Elisa mwana wa Safati, ndipo anam’peza akulima ndi pulawo+ yokokedwa ndi ng’ombe ziwiri zamphongo. Panali mapulawo 12 oterowo ndipo pulawo yake inali kumbuyo kwa onsewo. Choncho Eliya anapita pamene panali Elisa n’kumuponyera chovala chake chauneneri.+
-