1 Akorinto 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu. Aheberi 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso, kodi Mulungu ananyansidwa ndi ndani kwa zaka 40?+ Kodi sananyansidwe ndi anthu amene anachimwa aja, amene anafera m’chipululu?+
5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu.
17 Komanso, kodi Mulungu ananyansidwa ndi ndani kwa zaka 40?+ Kodi sananyansidwe ndi anthu amene anachimwa aja, amene anafera m’chipululu?+