Numeri 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma anthu onse amene aona ulemerero wanga,+ ndi zizindikiro zanga+ zimene ndinachita ku Iguputo, ndi zimene ndachita m’chipululu, amene akupitirizabe kundiyesa+ maulendo 10 onsewa, amenenso sanamvere mawu anga,+ Numeri 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+ 1 Akorinto 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu. 1 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo. Yuda 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+
22 Koma anthu onse amene aona ulemerero wanga,+ ndi zizindikiro zanga+ zimene ndinachita ku Iguputo, ndi zimene ndachita m’chipululu, amene akupitirizabe kundiyesa+ maulendo 10 onsewa, amenenso sanamvere mawu anga,+
29 Mitembo yanu idzagona m’chipululu muno,+ nonsenu amene munawerengedwa, kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, inu amene mwakhala mukudandaula motsutsana nane.+
5 Ngakhale zinali choncho, ambiri a iwo Mulungu sanakondwere+ nawo, ndipo anathana+ nawo m’chipululu.
10 Tisakhalenso ong’ung’udza, mmene ena mwa iwo anang’ung’udzira,+ wowonongayo+ n’kuwawononga onsewo.
5 Ngakhale kuti mukudziwa kale zinthu zonse, ndikufuna kukukumbutsani kuti,+ ngakhale kuti Yehova anapulumutsa anthu ake powatulutsa m’dziko la Iguputo,+ pambuyo pake anawononga amene analibe chikhulupiriro.+