Ekisodo 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Samala ndipo umvere mawu ake. Usam’pandukire, chifukwa sadzalekerera zolakwa zanu,+ pakuti dzina langa lili mwa iye. Numeri 14:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 amuna amene anadzanena zoipa zokhazokha zokhudza dzikolo, adzafa ndi mliri wa Yehova.+
21 Samala ndipo umvere mawu ake. Usam’pandukire, chifukwa sadzalekerera zolakwa zanu,+ pakuti dzina langa lili mwa iye.