Ekisodo 12:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Amuna amphamvu oyenda pansi analipo pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+ Numeri 1:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 onse amene analembedwa mayina anakwana 603,550.+
37 Pamenepo ana a Isiraeli ananyamuka ku Ramese+ kupita ku Sukoti.+ Amuna amphamvu oyenda pansi analipo pafupifupi 600,000, osawerengera ana.+