Ekisodo 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamene mukupereka kwa Yehova chopereka chokuphimbirani machimo,+ anthu olemera asapereke zochuluka, ndipo osauka asapereke zosakwana hafu ya sekeli.+
15 Pamene mukupereka kwa Yehova chopereka chokuphimbirani machimo,+ anthu olemera asapereke zochuluka, ndipo osauka asapereke zosakwana hafu ya sekeli.+