Yobu 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+ Miyambo 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu wolemera ndiponso munthu wosauka n’chimodzimodzi.+ Amene anapanga onsewa ndi Yehova.+ Aefeso 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu ambuye, muzichitiranso akapolo anu chimodzimodzi ndipo muleke kuwaopseza,+ pakuti mukudziwa kuti Ambuye wa nonsenu, wa iwowo ndi wa inuyo,+ ali kumwamba ndipo alibe tsankho.+
19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+
9 Inu ambuye, muzichitiranso akapolo anu chimodzimodzi ndipo muleke kuwaopseza,+ pakuti mukudziwa kuti Ambuye wa nonsenu, wa iwowo ndi wa inuyo,+ ali kumwamba ndipo alibe tsankho.+