-
Yoswa 7:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mawa m’mawa, mubwere fuko ndi fuko. Fuko limene Yehova adzasankhe+ lidzabwere patsogolo. Kenako mbumba ndi mbumba, ndipo mbumba imene Yehova adzasankhe idzabwere patsogolo. Kenako banja ndi banja, ndipo banja limene Yehova adzasankhe lidzabwere patsogolo, komanso mwamuna aliyense wamphamvu payekhapayekha.
-