1 Samueli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani mʼmasautso anu onse ndiponso mʼmavuto anu, ndipo munanena kuti: “Ayi, mutisankhire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova potengera mafuko anu ndiponso mabanja anu.’”*
19 Koma lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani mʼmasautso anu onse ndiponso mʼmavuto anu, ndipo munanena kuti: “Ayi, mutisankhire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova potengera mafuko anu ndiponso mabanja anu.’”*