19 Koma inu, lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani m’masautso anu onse ndi m’zowawa zanu, kufika ponena kuti: “Ife tikufuna kuti utiikire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova malinga ndi mafuko anu+ ndi mabanja anu.’”