Yeremiya 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anakonzekera kumuthira nkhondo ndipo anati:+ “Nyamukani, tiyeni tipite dzuwa lili paliwombo!”+ “Tsoka ife chifukwa nthawi yatithera ndipo zithunzithunzi zikupitiriza kutalika!” Yoweli 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Anthu inu, lengezani pakati pa mitundu ina kuti,+ ‘Konzekerani nkhondo! Konzekeretsani amuna amphamvu!+ Amuna onse ankhondo abwere!+
4 Anakonzekera kumuthira nkhondo ndipo anati:+ “Nyamukani, tiyeni tipite dzuwa lili paliwombo!”+ “Tsoka ife chifukwa nthawi yatithera ndipo zithunzithunzi zikupitiriza kutalika!”
9 “Anthu inu, lengezani pakati pa mitundu ina kuti,+ ‘Konzekerani nkhondo! Konzekeretsani amuna amphamvu!+ Amuna onse ankhondo abwere!+