Ezekieli 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, iwe ndikulanga ndi kuwononga ngalande zako zotuluka mu Nailo.+ Dziko la Iguputo ndiliwononga. Ndilisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ kukafika kumalire a dziko la Itiyopiya. Ezekieli 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova wanena kuti, ‘Nawonso othandiza Iguputo adzaphedwa, ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.’+ “‘Kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,+ anthu adzaphedwa ndi lupanga m’dzikolo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
10 Choncho, iwe ndikulanga ndi kuwononga ngalande zako zotuluka mu Nailo.+ Dziko la Iguputo ndiliwononga. Ndilisandutsa malo ouma komanso bwinja,+ kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene+ kukafika kumalire a dziko la Itiyopiya.
6 “Yehova wanena kuti, ‘Nawonso othandiza Iguputo adzaphedwa, ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.’+ “‘Kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,+ anthu adzaphedwa ndi lupanga m’dzikolo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.